-
Ekisodo 22:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ngati munthu wayatsa moto, motowo nʼkugwirira zomera zaminga ndipo wafalikira mʼmunda wa munthu wina nʼkuwotcha mitolo yambewu, mbewu zosadula kapena munda wonse, amene anayatsa motowo azilipira mbewu zimene zapsazo.
-