Ekisodo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngati munthu wapatsa mnzake ndalama kapena katundu wina kuti amusungire, zinthuzo nʼkubedwa mʼnyumba ya mnzakeyo, wakubayo akapezeka azilipira zowirikiza kawiri.+
7 Ngati munthu wapatsa mnzake ndalama kapena katundu wina kuti amusungire, zinthuzo nʼkubedwa mʼnyumba ya mnzakeyo, wakubayo akapezeka azilipira zowirikiza kawiri.+