Ekisodo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati wakubayo sanapezeke, azibweretsa mwininyumbayo pamaso pa Mulungu woona*+ kuti zidziwike ngati iyeyo ndi amene waba katundu wa mnzakeyo kapena ayi.
8 Ngati wakubayo sanapezeke, azibweretsa mwininyumbayo pamaso pa Mulungu woona*+ kuti zidziwike ngati iyeyo ndi amene waba katundu wa mnzakeyo kapena ayi.