-
Ekisodo 22:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Pa milandu yonse yokhudza kutenga chinthu cha mwini popanda chilolezo, kaya ndi ngʼombe, bulu, nkhosa, chovala kapena chilichonse chimene chinasowa chomwe angachiloze kuti, ‘Ichi nʼchanga!’ awiri onsewo mlandu wawo uzifika pamaso pa Mulungu woona.+ Amene Mulungu adzamuweruze kuti ndi wolakwa, azilipira mnzakeyo zowirikiza kawiri.+
-