-
Ekisodo 22:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ngati munthu wapatsa mnzake bulu, ngʼombe, nkhosa kapena chiweto chilichonse kuti amusungire, ndipo chafa kapena chavulala kwambiri kapenanso chagwidwa popanda munthu kuona zimene zachitika,
-