-
Ekisodo 22:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ngati chiwetocho chinaphedwa ndi chilombo, azibweretsa chiweto chakufacho monga umboni. Iye sakuyenera kulipira ngati chiweto chaphedwa ndi chilombo.
-