Ekisodo 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musamachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kumʼpondereza,+ chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+
21 Musamachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kumʼpondereza,+ chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+