-
Ekisodo 22:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Mkwiyo wanga udzakuyakirani ndipo ndidzakuphani ndi lupanga, moti akazi anu adzakhala akazi amasiye ndipo ana anu adzakhala ana amasiye.
-