Ekisodo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa chofunda chake nʼchomwecho. Ndi nsalu imene amafunda.+ Nanga afunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamva ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:27 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2017, tsa. 9
27 Chifukwa chofunda chake nʼchomwecho. Ndi nsalu imene amafunda.+ Nanga afunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamva ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+