Ekisodo 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Musamazengereze kundipatsa nsembe kuchokera pa zokolola zanu zomwe ndi zambiri komanso kuchokera ku vinyo ndi mafuta omwe ndi ochuluka.+ Mwana wanu wamwamuna woyamba kubadwa muzimupereka kwa ine.+
29 Musamazengereze kundipatsa nsembe kuchokera pa zokolola zanu zomwe ndi zambiri komanso kuchokera ku vinyo ndi mafuta omwe ndi ochuluka.+ Mwana wanu wamwamuna woyamba kubadwa muzimupereka kwa ine.+