Ekisodo 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mukaona bulu wa munthu wodana nanu atagona pansi chifukwa cholemedwa ndi katundu, munthu wodana nanuyo musamamusiye yekha. Muzimuthandiza kumasula katunduyo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:5 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 195
5 Mukaona bulu wa munthu wodana nanu atagona pansi chifukwa cholemedwa ndi katundu, munthu wodana nanuyo musamamusiye yekha. Muzimuthandiza kumasula katunduyo.+