Ekisodo 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamapondereze mlendo amene akukhala nanu. Inu mukudziwa mmene zimakhalira ukakhala mlendo, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2016, tsa. 9
9 Musamapondereze mlendo amene akukhala nanu. Inu mukudziwa mmene zimakhalira ukakhala mlendo, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+