Ekisodo 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Inu musanafike, ndidzachititsa anthuwo mantha*+ ndipo Ahivi, Akanani ndi Ahiti adzathawiratu pamaso panu.+
28 Inu musanafike, ndidzachititsa anthuwo mantha*+ ndipo Ahivi, Akanani ndi Ahiti adzathawiratu pamaso panu.+