Ekisodo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Mulungu anauza Mose kuti: “Kwera mʼphiri upite kwa Yehova, iweyo, Aroni, Nadabu, Abihu+ ndi akulu 70 a Isiraeli, ndipo mukagwade chapatali.
24 Kenako Mulungu anauza Mose kuti: “Kwera mʼphiri upite kwa Yehova, iweyo, Aroni, Nadabu, Abihu+ ndi akulu 70 a Isiraeli, ndipo mukagwade chapatali.