Ekisodo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Mose analemba mawu onse a Yehova.+ Ndiyeno anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkukamanga guwa lansembe ndi zipilala 12 zoimira mafuko 12 a Isiraeli, mʼmunsi mwa phiri.
4 Choncho Mose analemba mawu onse a Yehova.+ Ndiyeno anadzuka mʼmawa kwambiri nʼkukamanga guwa lansembe ndi zipilala 12 zoimira mafuko 12 a Isiraeli, mʼmunsi mwa phiri.