Ekisodo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anatuma Aisiraeli achinyamata ndipo iwo anapereka nsembe zopsereza komanso anapereka ngʼombe kuti zikhale nsembe zamgwirizano+ zoperekedwa kwa Yehova.
5 Kenako anatuma Aisiraeli achinyamata ndipo iwo anapereka nsembe zopsereza komanso anapereka ngʼombe kuti zikhale nsembe zamgwirizano+ zoperekedwa kwa Yehova.