Ekisodo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anatenga buku la pangano nʼkuwerengera anthuwo mokweza.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:7 Nsanja ya Olonda,5/1/1995, ptsa. 9, 113/1/1995, tsa. 11
7 Kenako anatenga buku la pangano nʼkuwerengera anthuwo mokweza.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+