Ekisodo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kwera mʼphiri muno ufike kwa ine ndipo ukhalebe momʼmuno. Ndikupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+
12 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Kwera mʼphiri muno ufike kwa ine ndipo ukhalebe momʼmuno. Ndikupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+