Ekisodo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mose ndi Yoswa mtumiki wake ananyamuka,+ ndipo Mose anakwera mʼphiri la Mulungu woona.+