Ekisodo 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mose anauza akuluwo kuti: “Tidikireni pompano mpaka titabwerako.+ Muli ndi Aroni ndi Hura,+ ndiye aliyense amene ali ndi mlandu wofuna kuweruzidwa azipita kwa iwowa.”+
14 Koma Mose anauza akuluwo kuti: “Tidikireni pompano mpaka titabwerako.+ Muli ndi Aroni ndi Hura,+ ndiye aliyense amene ali ndi mlandu wofuna kuweruzidwa azipita kwa iwowa.”+