Ekisodo 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ulemerero wa Yehova+ unakhalabe paphiri la Sinai,+ ndipo mtambowo unakuta phirilo kwa masiku 6. Pa tsiku la 7, Mulungu anaitana Mose kuchokera mumtambowo.
16 Ulemerero wa Yehova+ unakhalabe paphiri la Sinai,+ ndipo mtambowo unakuta phirilo kwa masiku 6. Pa tsiku la 7, Mulungu anaitana Mose kuchokera mumtambowo.