Ekisodo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso ulandire miyala ya onekisi ndi miyala ina yoika pa efodi+ ndiponso pachovala pachifuwa.+