-
Ekisodo 25:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mulipangire mphete 4 zagolide ndi kuziika pamwamba pa miyendo yake 4. Mphete ziwiri zikhale mbali imodzi, ndipo mphete zina ziwiri zikhale mbali inayo.
-