Ekisodo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mupangenso ndodo zonyamulira za mtengo wa mthethe nʼkuzikuta ndi golide.+