-
Ekisodo 25:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Mphindi imodzi ikhale pansi pa nthambi zake ziwiri zoyambirira. Mphindi ina ikhalenso pansi pa nthambi zake ziwiri, ndipo mphindi inanso ikhale pansi pa nthambi zinanso ziwiri. Zikhale choncho ndi nthambi 6 zotuluka muthunthu la choikapo nyale.
-