Ekisodo 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Nsalu yotchinga* khomo la chihema uipangire zipilala 5 za mtengo wa mthethe zokutidwa ndi golide. Tizitsulo tokolowekapo nsaluyo tikhale tagolide. Ndipo upange zitsulo 5 zakopa zokhazikapo zipilalazo.”
37 Nsalu yotchinga* khomo la chihema uipangire zipilala 5 za mtengo wa mthethe zokutidwa ndi golide. Tizitsulo tokolowekapo nsaluyo tikhale tagolide. Ndipo upange zitsulo 5 zakopa zokhazikapo zipilalazo.”