Ekisodo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Utenge miyala iwiri ya onekisi+ nʼkulembapo mayina a ana a Isiraeli mochita kugoba.+