Ekisodo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mmisiri wogoba agobe mayina a ana a Isiraeli pamiyala iwiriyo ngati mmene amagobera chidindo.+ Kenako miyalayo idzaikidwe mʼzoikamo zake zagolide.
11 Mmisiri wogoba agobe mayina a ana a Isiraeli pamiyala iwiriyo ngati mmene amagobera chidindo.+ Kenako miyalayo idzaikidwe mʼzoikamo zake zagolide.