Ekisodo 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Udzalowetse miyala iwiriyo pansalu zamʼmapewa za efodi kuti ikhale miyala ya chikumbutso cha ana a Isiraeli.+ Poonekera kwa Yehova, Aroni azidzanyamula mayina awo pansalu ziwiri zamʼmapewa ake kuti chikhale chikumbutso.
12 Udzalowetse miyala iwiriyo pansalu zamʼmapewa za efodi kuti ikhale miyala ya chikumbutso cha ana a Isiraeli.+ Poonekera kwa Yehova, Aroni azidzanyamula mayina awo pansalu ziwiri zamʼmapewa ake kuti chikhale chikumbutso.