Ekisodo 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndi matcheni awiri agolide woyenga bwino. Uwapange ngati zingwe zopota+ mwaluso, ndipo ulumikize matcheni okhala ngati zingwewo ku zoikamo miyala.+
14 ndi matcheni awiri agolide woyenga bwino. Uwapange ngati zingwe zopota+ mwaluso, ndipo ulumikize matcheni okhala ngati zingwewo ku zoikamo miyala.+