Ekisodo 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ukachipinda pakati mbali zake zonse 4 zizifanana, mulitali mwake chikhale masentimita 22* ndipo mulifupi mwake masentimita 22.
16 Ukachipinda pakati mbali zake zonse 4 zizifanana, mulitali mwake chikhale masentimita 22* ndipo mulifupi mwake masentimita 22.