-
Ekisodo 28:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Miyalayo uiike malinga ndi mayina a ana 12 a Isiraeli. Mwala uliwonse aulembe mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo ndipo mwala uliwonse ukhale ndi dzina limodzi mwa mayina a mafuko 12.
-