-
Ekisodo 28:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Upange mphete ziwiri zagolide nʼkuziika pachovala pachifuwa. Mphete ziwirizo uziike mʼmakona awiri a chovala pachifuwacho.
-