Ekisodo 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Upange mphete ziwiri zagolide nʼkuziika mʼmakona awiri a chovala pachifuwa kumbali yamkati yokhudzana ndi efodi.+
26 Upange mphete ziwiri zagolide nʼkuziika mʼmakona awiri a chovala pachifuwa kumbali yamkati yokhudzana ndi efodi.+