Ekisodo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Upangenso mphete zina ziwiri zagolide nʼkuziika kutsogolo kwa efodi, mʼmunsi mwa nsalu ziwiri zamʼmapewa, pafupi ndi polumikizira, pamwamba pa lamba woluka* wa efodi.+
27 Upangenso mphete zina ziwiri zagolide nʼkuziika kutsogolo kwa efodi, mʼmunsi mwa nsalu ziwiri zamʼmapewa, pafupi ndi polumikizira, pamwamba pa lamba woluka* wa efodi.+