Ekisodo 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chovala pachifuwacho achimange ndi chingwe chabuluu. Chingwe chimenecho chilowe mumphete za chovala pachifuwa komanso mphete za efodi. Zimenezi zidzathandiza kuti chovala pachifuwacho chisasunthe koma chizikhala pamwamba pa lamba woluka* wa efodi.
28 Chovala pachifuwacho achimange ndi chingwe chabuluu. Chingwe chimenecho chilowe mumphete za chovala pachifuwa komanso mphete za efodi. Zimenezi zidzathandiza kuti chovala pachifuwacho chisasunthe koma chizikhala pamwamba pa lamba woluka* wa efodi.