-
Ekisodo 28:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Aroni azinyamula mayina a ana a Isiraeli pamtima pake, pachovala pachifuwa chachiweruzo, akamalowa mʼMalo Oyera kuti chikhale chikumbutso pamaso pa Yehova nthawi zonse.
-