Ekisodo 28:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Upange malaya odula manja ovala mkati mwa efodi. Uwapange ndi ulusi wabuluu wokhawokha.+