-
Ekisodo 28:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Malayawo akhale otsegula pamwamba pake, pakatikati. Potsegulapo pakhale popenderera mʼmphepete mwake ndi nsalu yowomba. Pakhale potsegula ngati chovala chakunkhondo chamamba achitsulo, kuti chisangʼambike.
-