Ekisodo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mumpendero wake wamʼmunsi upangemo zinthu zooneka ngati makangaza* za ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo ndi ulusi wofiira kwambiri kuzungulira mpenderowo. Upangenso mabelu agolide pakati pa makangazawo kuzungulira mpenderowo.
33 Mumpendero wake wamʼmunsi upangemo zinthu zooneka ngati makangaza* za ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo ndi ulusi wofiira kwambiri kuzungulira mpenderowo. Upangenso mabelu agolide pakati pa makangazawo kuzungulira mpenderowo.