-
Ekisodo 28:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Uziika belu lagolide kenako khangaza, belu lagolide kenako khangaza kuzungulira mpendero wamʼmunsi mwa malaya odula manjawo.
-