Ekisodo 28:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Aroni azivala malayawo kuti atumikire, ndipo mabeluwo azimveka iye akamalowa mʼmalo opatulika pamaso pa Yehova komanso akamatuluka, kuti asafe.+
35 Aroni azivala malayawo kuti atumikire, ndipo mabeluwo azimveka iye akamalowa mʼmalo opatulika pamaso pa Yehova komanso akamatuluka, kuti asafe.+