Ekisodo 28:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri ndiponso uluke lamba wa mkanjo.+
39 Uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri ndiponso uluke lamba wa mkanjo.+