Ekisodo 28:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ana a Aroni uwapangirenso mikanjo, malamba ndi mipango* yokulunga kumutu+ kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+
40 Ana a Aroni uwapangirenso mikanjo, malamba ndi mipango* yokulunga kumutu+ kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+