Ekisodo 28:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Uveke Aroni mʼbale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwayeretse nʼkuwaika*+ kuti atumikire monga ansembe anga.
41 Uveke Aroni mʼbale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwayeretse nʼkuwaika*+ kuti atumikire monga ansembe anga.