Ekisodo 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aroni ndi ana ake adye+ nyama ya nkhosayo ndi mkate umene uli mʼdengu, adyere pakhomo la chihema chokumanako.
32 Aroni ndi ana ake adye+ nyama ya nkhosayo ndi mkate umene uli mʼdengu, adyere pakhomo la chihema chokumanako.