Ekisodo 29:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Uzipereka ngʼombe ya nsembe yamachimo tsiku lililonse kuti iphimbe machimo. Uziyeretsa guwa lansembe ku machimo poliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza kuti likhale loyera.+
36 Uzipereka ngʼombe ya nsembe yamachimo tsiku lililonse kuti iphimbe machimo. Uziyeretsa guwa lansembe ku machimo poliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza kuti likhale loyera.+