Ekisodo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ukamachita kalembera wa ana a Isiraeli,+ aliyense azipereka dipo la moyo wake kwa Yehova pa nthawi imene ukuwawerengayo. Azichita zimenezi kuti mliri usawagwere pochita kalemberayo. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:12 Nsanja ya Olonda,11/1/2011, tsa. 12
12 “Ukamachita kalembera wa ana a Isiraeli,+ aliyense azipereka dipo la moyo wake kwa Yehova pa nthawi imene ukuwawerengayo. Azichita zimenezi kuti mliri usawagwere pochita kalemberayo.