Ekisodo 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Azisamba mʼmanja ndi mapazi awo kuti asafe. Limeneli ndi lamulo kwa iwo mpaka kalekale, likhale lamulo kwa Aroni ndi ana ake ku mibadwo yawo yonse.”+
21 Azisamba mʼmanja ndi mapazi awo kuti asafe. Limeneli ndi lamulo kwa iwo mpaka kalekale, likhale lamulo kwa Aroni ndi ana ake ku mibadwo yawo yonse.”+