Ekisodo 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kenako utenge mafuta onunkhira, abwino kwambiri awa: mule* woundana wokwana masekeli 500, sinamoni wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi wonunkhira wokwana masekeli 250.
23 “Kenako utenge mafuta onunkhira, abwino kwambiri awa: mule* woundana wokwana masekeli 500, sinamoni wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi wonunkhira wokwana masekeli 250.